Yesaya 38:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku amenewo Hezekiya anadwala, nafuna kufa. Ndipo Yesaya mneneri, mwana wa Amozi, anadza kwa iye, nati kwa iye, Atero Yehova, Konza nyumba yako, pakuti iwe udzafa, sudzakhala ndi moyo.

Yesaya 38

Yesaya 38:1-6