Yesaya 37:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamva anthu alinkunena za Tiraka, mfumu ya Kusi, Iye waturuka kudzamenyana ndi iwe. Ndipo pamene anamva, iye anatumiza mithenga kwa Hezekiya ndi kuti,

Yesaya 37

Yesaya 37:1-18