Yesaya 37:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wa Yehova anaturuka, naphaipha m'zitando za Asuri, zikwi zana ndi makumi asanu ndi atatu ndi zisanu, ndipo pamene anthu anauka mamawa, taonani, onse ndiwo mitembo.

Yesaya 37

Yesaya 37:31-38