Yesaya 37:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya analandira kalatayo m'manja mwa mithengayo, namuwerenga; ndipo Hezekiya anakwera kunka ku nyumba ya Yehova, namfunyulula pamaso pa Yehova.

Yesaya 37

Yesaya 37:9-15