Yesaya 37:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene mfumu Hezekiya anamva, anang'amba zobvala zace, nabvala ciguduli, nalowa m'nyumba ya Yehova.

Yesaya 37

Yesaya 37:1-10