Yesaya 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace upereketu zikole kwa mbuyanga, mfumu ya Asuri, ndipo ine ndidzakupatsa iwe akavalo zikwi ziwiri, ngati iwe udzaona okwerapo.

Yesaya 36

Yesaya 36:1-10