Yesaya 36:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kazembeyo anati kwa iwo, Nenani inu tsopano kwa Hezekiya, Itero mfumu yaikuru, mfumu ya Asuri, Kodi cikhulupiriro ici ncotani, ucikhulupirira iwe?

Yesaya 36

Yesaya 36:1-5