Yesaya 36:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa milungu yonse ya maiko awa, inapulumutsa dziko lao m'manja mwanga ndi iti, kuti Yehova adzapulumutsa Yerusalemu m'manja mwanga?

Yesaya 36

Yesaya 36:17-22