Yesaya 36:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cenjerani angakukopeni inu Hezekiya, ndi kuti, Yehova adzatipulumutsa ife. Kodi milungu iri yonse ya amitundu inapulumutsa dziko lao m'manja mwa mfumu ya ku Asuri?

Yesaya 36

Yesaya 36:14-22