Yesaya 35:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nenani kwa a mitima ya cinthenthe, Limbani, musaope; taonani, Mulungu wanu adza ndi kubwezera cilango, ndi mphotho ya Mulungu; Iye adzafika ndi kukupulumutsani.

Yesaya 35

Yesaya 35:1-10