Yesaya 34:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo makamu onse a kumwamba adzasungunuka, ndi miyamba idzapindika pamodzi ngati mpukutu; makamu ao onse adzafota monga tsamba limafota pampesa ndi kugwa, ndi monga tsamba lifota pamkuyu.

Yesaya 34

Yesaya 34:1-10