Yesaya 34:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova akwiyira amitundu onse, nacitira ukali khamu lao lonse; Iye wawaononga psiti, wawapereka kukaphedwa,

Yesaya 34

Yesaya 34:1-10