Yesaya 34:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumeneko njoka yotumpha idzapanga cisanja cace, niikira, niumatira, niswa mumthunzi mwace; inde kumeneko miimba idzasonkhana wonse ndi unzace.

Yesaya 34

Yesaya 34:8-17