Yesaya 34:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sadzazimikai usiku, ngakhale usana; utsi wace udzakwera nthawi zonse; m'mibadwo mibadwo lidzakhala labwinja, palibe amene adzapitapo nthawi za nthawi.

Yesaya 34

Yesaya 34:3-15