Yesaya 33:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ocimwa a m'Ziyoni ali ndi mantha, kunthunthumira kwadzidzimutsa anthu opanda Mulungu. Ndani mwa ife adzakhala ndi moto Wakunyeketsa? ndani mwa ife adzakhala ndi zotentha zacikhalire?

Yesaya 33

Yesaya 33:4-22