Yesaya 32:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wopusa adzanena zopusa, ndi mtima wace udzacita mphulupulu, kucita zoipitsa, ndi kunena za Yehova molakwira, kusowetsa konse mtima wanjala, ndi kulepheretsa cakumwa ca waludzu.

Yesaya 32

Yesaya 32:3-9