Yesaya 32:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu adzakhala monga pobisalira mphepo, ndi pousira cimphepo; monga mitsinje yamadzi m'malo ouma, monga mthunzi wa thanthwe lalikuru m'dziko lotopetsa.

Yesaya 32

Yesaya 32:1-5