Yesaya 32:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi nchito ya cilungamo idzakhala mtendere; ndi zotsata cilungamo zidzakhala mtendere, ndi kukhulupirika ku nthawi zonse.

Yesaya 32

Yesaya 32:10-18