Yesaya 32:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti nyumba ya mfumu idzasiyidwa; mudzi wa anthu ambiri udzakhala bwinja; citunda ndi nsanja zidzakhala nkhwimba ku nthawi zonse, pokondwera mbidzi podyera zoweta;

Yesaya 32

Yesaya 32:4-20