Yesaya 30:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo onse adzakhala ndi manyazi, ndi anthu amene sangapindule nao kanthu, amene sakhala kwa iwo thangata, pena phindu, koma manyazi ndi citonzo.

Yesaya 30

Yesaya 30:4-15