Yesaya 30:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamwamba pa mapiri akuru onse, ndipa zitunda zonse zazitaritari padzakhala mitsinje ndi micerenje ya madzi, tsiku lophana lalikuru, pamene nsanja zidzagwa.

Yesaya 30

Yesaya 30:20-31