Yesaya 30:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene ayenda kutsikira ku Aigupto, osafunsa kukamwa kwanga, kudzilimbitsa iwo okha ndi li mphamvu za Farao, ndi kukhulupirira mthunzi wa Aigupto

Yesaya 30

Yesaya 30:1-10