Yesaya 30:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anthu adzakhala m'Ziyoni pa Yerusalemu; iwe sudzaliranso, Iye ndithu adzakukomera mtima pakumveka kupfuula kwako; pakumva Iye adzayankha.

Yesaya 30

Yesaya 30:14-29