Yesaya 30:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace kuipa kumeneku kudzakhala kwa inu monga pogumuka pofuna kugwa, monga potukuka m'khoma lalitari, kugumuka kwace kufika modzidzimutsa dzidzidzi.

Yesaya 30

Yesaya 30:5-17