Yesaya 29:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzamanga zithando kuzungulira iwe ponse, ndipo ndidzamanga linga ndi kuunjika miulu yakumenyanirana ndi iwe.

Yesaya 29

Yesaya 29:1-4