Yesaya 29:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka kwa iwo amene afunitsa kubisira Yehova uphungu wao, ndi nchito zao ziri mumdima, ndipo amati Ndani ationa ife? ndani atidziwa ife?

Yesaya 29

Yesaya 29:11-16