Yesaya 28:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi duwa lakufota la ulemerero wace wokongola, limene liri pamutu pa cigwa ca nthaka yabwino, lidzakhala ngati nkhuyu yoyamba kuca malimwe asanafike; polona wakupenya imeneyo, amaidya iri m'dzanja lace.

Yesaya 28

Yesaya 28:1-10