Yesaya 28:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Ambuye ali ndi wina wamphamvu wolimba; ngati cimphepo ca matalala, mkuntho wakuononga, ngati namondwe wa madzi amphamvu osefukira, adzagwetsa pansi ndi dzanja lamphamvu.

Yesaya 28

Yesaya 28:1-8