Yesaya 28:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace Ambuye Yehova atero, Taonani, ndiika m'Ziyoni mwala wa maziko, mwala woyesedwa mwala wa pangondya, wa mtengo wace wokhazikika ndithu; wokhulupirira sadzafulumira.

Yesaya 28

Yesaya 28:15-19