Yesaya 27:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Mulungu wakantha Yakobo, monga umo anawakanthira akumkanthawo? kapena kodi iye waphedwa malinga ndi kuphedwa kwa iwo amene anaphedwa ndi iye?

Yesaya 27

Yesaya 27:1-11