Yesaya 26:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti taonani, Yehova adza kucokera ku malo ace kudzazonda okhala pa dziko lapansi, cifukwa ca kuipa kwao; dziko lidzabvumbulutsa mwazi wace, ndipo silidzabvundikiranso ophedwa ace.

Yesaya 26

Yesaya 26:18-21