Yesaya 26:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova, dzanja lanu litukulidwa, koma iwo saona; koma iwo adzaona cangu canu ca kwa anthu, nadzakhala ndi manyazi; inde moto udzamariza adani anu.

Yesaya 26

Yesaya 26:6-19