Yesaya 24:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzikonso laipitsidwa ndi okhalamo ace omwe, cifukwa iwo alakwa pamalamulo nasinthanitsa malemba, natyola cipangano ca nthawi zonse.

Yesaya 24

Yesaya 24:1-12