Yesaya 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndi tsiku laphokoso, ndi lopondereza pansi, ndi lothetsa nzeru, locokera kwa Ambuye Yehova wa makamu, m'cigwa ca masomphenya, kugumuka kwa malinga, ndi kupfuulira kumapiri.

Yesaya 22

Yesaya 22:1-6