Yesaya 22:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaika mfungulo wa nyumba ya Davide paphewa pace, ndipo iye adzatsegula, ndipo palibe wina adzatseka, iye adzatseka ndipo palibe wina adzatsegula.

Yesaya 22

Yesaya 22:14-25