Yesaya 22:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ucitanji iwe kuno, ndimo ndani ali nawe kuno, kuti iwe wagoba manda kuno, ndi kudzigobera manda pamwamba, ndi kudzisemera mogonamo m'thanthwe.

Yesaya 22

Yesaya 22:11-22