Yesaya 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anapfuulitsa ngati mkango, Ambuye inu, ine ndiimabe pamwamba pa nsanja nthawi ya usana, ndipo ndiikidwa mu ulonda wanga usiku wonse;

Yesaya 21

Yesaya 21:1-12