Yesaya 21:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masomphenya obvuta aonetsedwa kwa ine; wogula malonda wonyenga amangonyenga, ndi wofunkha amangofunkha. Kwera Elamu iwe; zunguniza Media iwe; kuusa moyo kwace konse ndakutonthoza.

Yesaya 21

Yesaya 21:1-11