Yesaya 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ambuye ana tero kwa ine, Cisanapite caka malinga ndi zaka za wolembedwa nchito ulemerero wonse wa Kedara udzagoma;

Yesaya 21

Yesaya 21:7-17