Yesaya 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti akalowe m'mapanga a m'matanthwe, ndi m'mindala a m'miyala, kuthawa kuopsya kwa Yehova, ndi ulemerero wacifumu wace, podzuka Iye kugwedeza dziko ndi mphamvu,

Yesaya 2

Yesaya 2:16-22