Yesaya 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu adzalowa m'mapanga a m'matanthwe, ndi m'maenje apansi, kuthawa kuopsya kwa Yehova, ndi ulemerero wacifumu wace, podzuka Iye kugwedeza dziko ndi mphamvu.

Yesaya 2

Yesaya 2:11-22