Yesaya 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maso a munthu akuyang'anira kumwamba adzatsitsidwa, ndi kudzikweza kwa anthu kudzaweramitsidwa pansi; ndipo Yehova yekha adzakwezedwa tsiku limenelo.

Yesaya 2

Yesaya 2:4-13