Yesaya 19:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzakantha Aigupto kukantha ndi kuciritsa; ndipo iwo adzabwerera kwa Yehova, ndipo Iye adzapembedzedwa ndi iwo, nadzawaciritsa.

Yesaya 19

Yesaya 19:20-25