Yesaya 19:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko la Yuda lidzaopsa Aigupto, yense wakulichula adzamtembenukira mwamantha, cifukwa ca uphungu wa Yehova wa makamu, aupanga pa dzikolo.

Yesaya 19

Yesaya 19:9-22