Yesaya 19:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa Aigupto.Taonani, Yehova wakwera pamwamba pa mtambo wothamanga, nadza ku Aigupto; ndi mafano a Aigupto adzagwedezeka pakufika kwace, ndi mtima wa Aigupto udzasungunuka pakati pace.

Yesaya 19

Yesaya 19:1-5