Yesaya 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kulira kwamveka kuzungulira malire a Moabu; kukuwa kwace kwafikira ku Eglaimu, ndi kukuwa kwace kwafikira ku Beerelimu.

Yesaya 15

Yesaya 15:1-9