Yesaya 15:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtima wanga upfuula cifukwa ca Moabu: akuru ace athawira ku Zoari, ku Eglatiselisiya; pakuti pa cikweza ca Luhiti akwera alikulira, pakuti m'njira ya Horanaimu akweza mpfuu wa cionongeko.

Yesaya 15

Yesaya 15:1-9