Yesaya 15:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'makwalala mwao adzimangira ciguduli m'cuuno, pamwamba pa nyumba zao, ndi m'malo a mabwalo ao, yense akuwa, naliritsa kwambiri.

Yesaya 15

Yesaya 15:1-8