Yesaya 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa Moabu.Pakuti usiku umodzi Ara wa ku Moabu wapasuka, nakhala cabe; usiku umodzi Kiri wa Moabu wapasuka, nakhala cabe.

Yesaya 15

Yesaya 15:1-4