Yesaya 14:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine ndidzawaukira, ati Yehova wa makamu, ndi kuononga ku Babulo dzina ndi otsala, ndi mwana wamwamuna, ndi cidzukulu cacimuna, ati Yehova.

Yesaya 14

Yesaya 14:12-28